Amalawi Akuyenda Okwiya Kwiya - Bon Kalindo

Описание к видео Amalawi Akuyenda Okwiya Kwiya - Bon Kalindo

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo insists he does not have a Facebook account, he also warns Malawi politicians to be considerate with how they run the affairs of Malawi and how they interact with Malawians because malawians have pent up anger due to the terrible state of affairs in Malawi.

Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo wanenetsa kuti alibe akaunti ya Facebook, wachenjezanso andale aku Malawi kuti aziganizira momwe amayendetsera dziko la Malawi ndi momwe amachitira ndi Amalawi chifukwa Amalawi akuyenda okiwaya kwiya.

#malawi

Комментарии

Информация по комментариям в разработке