FINCA Malawi Client Success Story - Brown Mwingiso

Описание к видео FINCA Malawi Client Success Story - Brown Mwingiso

Zaka zino, palibe kuyang’anira pansi businesi ina ili yonse. Kulimbikira, kuyitsata bwino bizinesi komanso kukhala pa ubale wabwino ndi FINCA Malawi ndiye chinsinsi chomwe ma bizinesi ena akutukukira. Mu zaka zochepa chabe, Shallom Wholesale ku Area 25 ku Lilongwe yapindula koposa ndipo ndiye Mponda Makwacha wathu mu tsiku la lero.
Kodi inu mukupanga malonda anji kwanuko? Tilankhuleni lero kuti nanunso muyambe kutukula bizinesi zanu ndi ngongole yathu.


𝐓𝐨 𝐚𝐩𝐩𝐥𝐲 𝐟𝐨𝐫 𝐚 𝐥𝐨𝐚𝐧:
🌐https://finca.mw/
📞Phone 312 kapena 0992 950 051
📲WhatsApp messages: +265 998638221


𝐊𝐮𝐭𝐢 𝐦𝐮𝐝𝐳𝐢𝐰𝐞 𝐳𝐚𝐦𝐛𝐢𝐫𝐢 𝐳𝐚 𝐅𝐈𝐍𝐂𝐀 𝐭𝐢𝐩𝐞𝐳𝐞𝐧𝐢 𝐩𝐚:


𝐅𝐚𝐜𝐞𝐛𝐨𝐨𝐤: https://web.facebook.com/FINCAMW


𝐖𝐡𝐚𝐭𝐬𝐀𝐩𝐩 𝐂𝐡𝐚𝐧𝐧𝐞𝐥: https://whatsapp.com/channel/0029VaJcT900w...


𝐋𝐢𝐧𝐤𝐞𝐝𝐈𝐧: https://mw.linkedin.com/company/finca-malawi


𝐘𝐨𝐮𝐓𝐮𝐛𝐞:    / @fincamw  


#FINCAForAll
#LetsGo!
#TiyeniKuFINCA
#BuildingTomorrowTogether

Комментарии

Информация по комментариям в разработке