Verse 1
Llama llama red pajama,
Hiphop si ndalama,
Chin’ganin’gani jr akuspita zima drama,
He claiming he a king,
Am like which village,
Chimidzi sichimatha it just keeps living,
How you a boss but a debt collector,
Bitch ways maybe you a transgender, swinging both ways,
Panza wabwanji ocheza sex offender,
I guess that’s why you say yu a G mi Brendah,
Street call you Gay gay A.K.A nfana wachimidzi kwao amamutcha okeyikeyi,
You get bread I get a cake baked,
Shhh quite he might think it’s a code for a gay fest,
Kutupikana siupanza osamanamiza mafana,
Ife timadya weight chigorilla chili ku nsana
Strategy mbola ku dissa kuti timutchule,
Beef yama gemu ati mimba ngati chule,
Kufuna kutchuka chidule mwafupa nazo chigule,
Chizungu ndi mbola chichewaso siungapindule,
Beef mwateleka koma simungayiphule,
This is a hiphop class bwela kuno tikusule,
Iwe ndi nkuku bwela kuno ndikudzule,
Mbewu yoyipa anadzala ndani tiyidule,
Flow kunyasa kuposa kunkhwapa kwa hule,
Wanamiza gulu apa ndiye ndi ulule,
Is this your king?
Is this your king?
My niggga,
You don’t want play with me,
You don’t want war with me,
Don’t start with me.
Verse 2
I thought I heard a bitch nigga say sumn,
On the internet claiming he stunning,
Talking about say he getting that money,
But on the low he ain’t making nothing,
Ife timavaya ku vephi eya,
Iwe ukadya nde kuti walanda katundu wa osapheya rent eya,
Ukhala bwanji og munthu nkamwa wangozazitsa zingwinjili,
Nangili,chain so fake material sungapangile ngakhale chibangili,
ukona mafi kwa akili,
Pachichewa tanthauzo lake ndi muobongo wangozazitsamo zimabibi,
Ngini ya mad di,
Flow mpaka thukuta kuyimba ndi tchito ya hard di,
Foul play muyitaneni Teddy amupase makadi di,
Hiphop yama G string,
Thigh cling,
Your king Is somebody else’s queen and sadly he a side ting,
Информация по комментариям в разработке