Kagulidwe Ka Ma share

Описание к видео Kagulidwe Ka Ma share

Isaac Zuze atiwuza momwe tingagulile ma share pa Malawi stock exchange. Mu video imeneyi , Isaac atifotokozela kuti ma share ndi chani, kodi ma broker amatani, mchifukwa chani tifunika ma brokerage account komanso tingayambe kugula ma share ndi ndalama zingati.

Комментарии

Информация по комментариям в разработке