Ndinu Oyera - RachealMusic

Описание к видео Ndinu Oyera - RachealMusic

This song is in Rachealmusic's Christ Revealed album as a worship medley. Ndinu Oyera is a phrase in Chewa, a language spoken in Zambia, Malawi and parts of Mozambique which means You are holy.

Ndinu oyera, Ndinu oyera, Ndinu oyera Yesu x4
(You are Holy, You are holy, You are holy, Jesus)

Poti munali, ndipo muli, ndipo muzhankala nthawi zonse, Ndinu oyera Yesu x2
(You who was, who is and will be forever, You are Holy, Jesus)

Ndinu wa mpanvu, Ndinu wa mpanvu, Ndinu wa mpanvu Yesu x2
(Omipotent, All powerful, You are mighty Jesus)

Poti munali, ndipo muli, ndipo muzhankala nthawi zonse, Ndinu wa mpanvu Yesu x2
(You who was, who is and will be forever, You are Holy, Jesus)

Oyera oyera oyera Ndinu Ambuye x6
(Holy Holy Holy are you Lord)

Kumwamba ndi Dziko lonse lidzala ndi ulemelero
(The heavens and the earth are filled with your glory)

Kumwamba ndi Dziko lonse ulemelero ni wanu Yehova
(In heaven and on earth all the glory belongs to you Jehovah)

Oyera oyera O Yehova mulungu wa mpanvu x7
(Holy Holy O Jehovah God almighty)

Комментарии

Информация по комментариям в разработке