'AMANDIYAMWISA MALISECHE DAILY '- MMWENYE AWUZA WA NTCHITO ADZIMUYAMWA MALISECHE

Описание к видео 'AMANDIYAMWISA MALISECHE DAILY '- MMWENYE AWUZA WA NTCHITO ADZIMUYAMWA MALISECHE

MMWENYE AWUMIRIZA WA NTCHITO KUTI AZIMUSEWERETSA MALISECHE
Kupeza ntchito ndi chinthu chokoma kwambiri kwa munthu aliyense makamaka uyo amene wakhala nthawi yayitali akuyisakasaka ndipo ali ndi anthu amene amadalira iyeyo monga makolo, ana komanso mkazi. Pamene munthu wapeza ntchito ndiye kuti amakhala ali ndi chiyembekezo chachikulu kuti zinthu zake zisintha ndipo amene amamudalirawa ayamba nawo kukondwa. Komatu zimenezi sizili motero kwa mkulu wina wochokera mu mzinda wa Lilongwe. Mkuluyu amene dzina lake sitilitchula anapeza ntchito yophika kwa mmwenye wina a Jayesh Kumar Dalwad amene anali wothandizira ntchito za mkulu wa kampani ya Shayona Cement Corporation ku Kanengo analibe malingaliro akuti chimwemwe chake chakuti wapeza ntchito chitha posachedwa ndikuyamba kukhala moyo wa mavuto.
Atakhala kwa nthawi yayitali asanapeze ntchito, mkuluyu amene amakhala kwa Mtsiriza mu mzindawu anali akukanika kusamalira ana ake atatu, koma mu mwezi wa January 2023, iye anapeza ntchito ngati wophika ku nyumba ya bwanayu imene ili ku malo amene kuli ma office a kampani ya Shayona yi ku Kanengo. Atangogwira ntchitoyo kwa mwezi umodzi, mwezi wotsatira wake umene ndi wa February zinthu zinayamba kusintha ndipo akuti abwana ake aja anayamba kumamawuza kuti adziwasisita bondo lawo.

Комментарии

Информация по комментариям в разработке