Msomba Ikawola Imodzi Mudengu Zonse Zawola - Bon Kalindo

Описание к видео Msomba Ikawola Imodzi Mudengu Zonse Zawola - Bon Kalindo

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo continues to say that he will not stop speaking the truth. He maintains his criticism of UTM and its leadership's membership in the Tonse Alliance. Today, he is responding to comments made by some UTM sympathizers about his audio released yesterday, in which he called for UTM to resign from the Tonse Alliance before telling Malawians that things are not okay in Malawi.

Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo apitiliza kunena kuti sasiya kulankhula zoona. Iye akutsutsabe UTM ndi utsogoleri wake mu Tonse Alliance. Lero akuyankha zomwe ena a chipani cha UTM adalankhula zokhuza audio yake yomwe adatulutsa dzulo pomwe adapempha UTM kuti ituluke mumgwirizano wa Tonse asadauze Amalawi kuti m’Malawi muno zinthu sizili bwino.

#malawi

Комментарии

Информация по комментариям в разработке