Mwina Tingosantha A Bon Kalindo Mu 2025 - Mzika Yokhudzidwa

Описание к видео Mwina Tingosantha A Bon Kalindo Mu 2025 - Mzika Yokhudzidwa

On Nyasa VoiceBox, a concerned citizen says that, in the absence of a viable government-in-waiting due to a weak opposition, activist Bon Kalindo may be our best option for president in Malawi come 2025.

Pa Nyasa VoiceBox, mzika yokhudzidwayi yati, womenyera ufulu wa anthu a Bon Kalindo atha kukhala mtsogoleri wabwino mu 2025 chifukwa wawonetsa kuti dziko lino amalikonda komaso amakhudzika ndi mavuto amene a Malawi akukumana nawo.

#malawi

Комментарии

Информация по комментариям в разработке