OYIMBA A KU MALAWI AKUPEZA NDALAMA ZINGATI PA YOUTUBE? - TILI NDI TOP 10

Описание к видео OYIMBA A KU MALAWI AKUPEZA NDALAMA ZINGATI PA YOUTUBE? - TILI NDI TOP 10

NOTE: Nthawi yomwe timapanga video yi tinayiwala Saint-Realest whose Estimated Monthly Earnings are at - $170 (MK294,627.68) - $2.7K (MK4,679,380.80)

Kupangira inu mukudabwa kuti Dr Namadingo sakupezeka bwanji pa list ya oyimba a ku Malawi amene akulandira ndalama zambiri kuchokera ku YouTube....List yi yapangidwa posakatula oyimba okhayo amene ali pa "YouTube Partner Program" kapena kuti oyimba amene anapanga monetize ndipo alibe ma strike aliwonse pa channel yawo to make money from youtube.

Malingana ndi kafukufuku amene anapangidwa pa YouTube Monetization Checker, zikuonetsa kuti pakali pano channel ya Dr Namadingo Monetization Status yake ili off zomwe zikutanthauza kuti sakulandira ndalama kuchoka ku YouTube pa zifukwa zomwe akudziwa a YouTube wo ndi Dr athu.

Komabe akanakhala kuti akulandira bobo ndekuti panopa bwezi Estimated Monthly Earnings ya Dr ili pa $395 (MK678,749.83) - $6.3K (130,423,068.60) zomwe zikanawaika Dr Numadingo pa number 3 pa oyimba a ku Malawi omwe akulandira ndalama zambiri kuchokera ku YouTube.

Комментарии

Информация по комментариям в разработке