Banja Lakumwamba Ndi Amayi Akumwamba | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu

Описание к видео Banja Lakumwamba Ndi Amayi Akumwamba | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu

Mulungu Adalenga Zonse Ndi
Chifuniro Chake. Kodi Chifuniro cha
Mulungu N'chiyani pa zenizeni za
Lamulo la Moyo?
Chifukwa chimene Mulungu
analengera zamoyo zonse padziko
lapansi pano kuti zilandire moyo
kudzera mwa mayi chinali
kutidziwitsa kuti moyo wosatha
umaperekedwa kudzera mwa Amayi
athu auzimu okha basi.
Chifukwa chimene Mulungu
anatiphunzitsira ife kuti Iye ndi
“Atate,” ndipo ife ndife ana ake
aamuna ndi aakazi akafuna
kuwulula Mulungu Amayi kupyolera
mu maudindo a aliyense m’banjamo.

Mamembala a Mpingo wa Mulungu
Ali ndi “Mapulani a Ufumu wa
Kumwamba,” chimene ndi, Kutsatira
Zimene Mulungu Amaphunzitsa.
Anthu amaona kuti n’kofunika
kukonzekera zopuma pantchito
pamene amakukhala ndi moyo waufupi
padziko lino lapansi. Koma kunena
zoona, n’kofunika kwambiri
kupanga mapulani ndi kukonzekera dziko
la angelo limene tidzakhalako kosatha.
Iwo amene akuyembekezadi ufumu
wakumwamba akulandira Atate
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu
Amayi amene abwera ngati
Apulumutsi mu m'badwo wa Mzimu
Woyera. Iwo amasunganso tsiku la
Sabata ndi Paskha wa pangano
latsopano monga ana a banja
lakumwamba.

Chivumbulutso 4:11
Muyenera inu, Ambuye wathu, ndi
Mulungu wathu, kulandira ulemerero ndi
ulemu ndi mphamvu; chifukwa
mudalenga zonse, ndipo mwa chifuniro
chanu zinakhala, ndipo zinalengedwa.


[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]

〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com

Комментарии

Информация по комментариям в разработке