Adzaletsa Kugura ndi kugulitsa Official HD 1080p 2

Описание к видео Adzaletsa Kugura ndi kugulitsa Official HD 1080p 2

Pamenepo, adzakuperekani, kunsautso nazakuphani. Anthu adzaperekana wina ndi nzake. Nkuthekatu Yemwe adzakupereke mmanja mwa adani ndi bwenzi lomwe umadya nalo limodzi. Pempherani pakuti ora loyesedwa lafika.

'ndi kuti munthu sangakhoze kugula kapena kugulitsa, koma iye yekha wakukhala nacho chilembo, ndilo dzina la chilombo, kapena chiwerengero cha dzina lake. '

CHIVUMBULUTSO 13:17
https://www.bible.com/bible/1708/REV....

Комментарии

Информация по комментариям в разработке