Chisankho Sichibeledwa Tsiku Lovota Imakhala Process - Bon Kalindo

Описание к видео Chisankho Sichibeledwa Tsiku Lovota Imakhala Process - Bon Kalindo

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo asks opposition parties to be vigilant ahead of the 2025 Elections. He also asks UTM members to sit down and have a soul searching meeting to reflect on where they are coming from and where they would like to go.

Ku Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo apempha zipani zotsutsa kuti zikhale tcheru pokonzekera zisankho za 2025. Apemphanso mamembala a UTM kuti akhale pansi nidkuganizira za komwe akuchokera ndi komwe akufuna kupita.

#malawi

Комментарии

Информация по комментариям в разработке