Mavuto apadziko lonse. Ndife anthu timafuna totakhala moyo | 7 may 2022

Описание к видео Mavuto apadziko lonse. Ndife anthu timafuna totakhala moyo | 7 may 2022

🌍 May 7 2022
15:00 GMT kuwulutsa kwa pompopompo.
Azilankhula zana zomasuliridwa pakamodzi.
Mayiko 180

MSONKHANO WAPADZIKOLONSE PA INTERNETI MAVUTO APADZILONSE. NDIFE ANTHU. TIMAFUNA KUKHALA MOYO POMPOPOMPO ndi ndinsli wawukulu womwe sunachitikepo, chithokozo chipite kwa anthu mazanazana omwe agwirizana mwapaokha makolo 180 pa nsanja la anthu odziwa kupanga zinthu. Zochitikazi zidzaulutsidwa pa masamba amchezo mazanazana padziko lonse. Izi zakozedwa ndi kukhazikitsidwa mwaulere ndi khama la anthu ongodzipereka ndikatundu wawo.

Nkhondo yomaliza ya umunthu yayamba tsopano. Iyitu ndi nkhondo yosaneneka. Kwa nthawi yoyamba mumbiri, anthu onse akukumana ndi mdani mmodzi wakunja. Mdani ameneyi ndi kusintha kwanyengo. Pakuthana ndi zoopsa pa dziko, mkofunikira kulungamitsa anthu onse pamodzi, chifukwa cha tsogolo la umunthu chifukwa ndife anthu amene timafuna titakhala ndi moyo.

Cholinga cha msonkhanowu ndikudziwitsa anthu onse moona mtima za kukula kwachiopsezo cha kusintha kwanyengo ndi ngozi za chilengedwe; pakuonetsa mulingo weniweni wa mavuto ankhaninkhani odza kamba ka mchitidwe owononga mmadera athu ndikuganizirapo mayankho othandiza kuthana ndi mavuto onse pakumanga gulu anthu opanga zinthu.

Ngati ndinu katswiri pa umodzi mwa mitu yafotokozedwayi, kapena ndinu mmodzi mwa amene mwakumanapo ndikuonapo nkhaza za mtundu owononga, ukapolo ndi mavuto a anthu othawa kwawo kapena ngati ndinu mboni ya tsoka la kusintha kwanyengo, chonde lumikazinani nafe. Wina aliyeseyo malinga kunena chilungamo.


Tikuitana anthu onse owona mtima ndi kusamala kuti atijoine kukozekera msonkhano kuyambira lero.

Kuti atengegawo pa msonkhano wapa dziko lonse ndikutenga mbali muzokonzekera, chonde lemberani ku:
[email protected]


Webusaiti yovomelezeka ya pulojekiti yapadziko lonse ANTHU OPANGA ZINTHU.
https://creative society.com

Msonkhano wapa internet pa dziko lonse "mavuto apadziko lonse nthawi ya chilungamo" Disembala 4, 2021 ndiziyankhulo zana zomasuliridwa pakamodzi:
https://creativesociety.com/global-cr...

#Anthu opanga zinthu
#mavutoapadzikolonse #tikufunakukhalamoyo

Комментарии

Информация по комментариям в разработке