Utumiki wa a Twaibu – za chakhumi. Kodi chili ndi ubwino wanji pa ife okhulupilira? Mverani.

Описание к видео Utumiki wa a Twaibu – za chakhumi. Kodi chili ndi ubwino wanji pa ife okhulupilira? Mverani.

Mu utumikiwu, a Twaibu akufotokoza za zomwe zimachitika pa munthu wopereka chakhumi moonadi. Akufotokoza izi pogwiritsa ntchito chidziwitso chawo ku chipembedzo cha satana komwe iwo akhalako kwa zaka zokwana 17.

Комментарии

Информация по комментариям в разработке