Mwinadi a Triephornia Mpinganjira adakwatiwa mcholinga chongofuna kusakaza chuma cha Bwanawa kapena.

Описание к видео Mwinadi a Triephornia Mpinganjira adakwatiwa mcholinga chongofuna kusakaza chuma cha Bwanawa kapena.

Kuchoka pamene Mayi Triephornia Benda adakwatiwa ndi Chikhwaya cha M'dziko La Malawi a Thomson Mpinganjira zaambiri zakhala zikukambidwa, ena mkumati mayiwa ndi Gold-digger chabe. kodi izi ndizoona? zambiri ziri mu video iyi.

yakonzedwa ku : https://265entmag.live/

Mukafuna kugula katundu wa origina okongoletsa khungu ochokera ku UK ma products monga body lotions, Serums, Body Creams, Deodorants ndi zina zambiri, ayankhuleni a Mastoura Cosmetics..

Tsamba lawo la Facebook lili apa https://web.facebook.com/profile.php?...

Iwowanso ali pa TikTok   / mastouracosmetic  

Комментарии

Информация по комментариям в разработке