JB " is the king of BEEF ku Malawi", ndipo anabwera kudza zindikilitsa gulu.

Описание к видео JB " is the king of BEEF ku Malawi", ndipo anabwera kudza zindikilitsa gulu.

Anthu ambiri amaona ngati JB ndiobalalika, komanso opoira. koma mu video iyiyi tikuona zomwe zimamupangitsa iyeyi kukhala star komanso katswiri mu rap industry ya Malawi.

Check out our website: https://265entmag.live/
Radio website: https://radio.265entmag.live/
Company website: https://agency.265entmag.live/

Комментарии

Информация по комментариям в разработке