Skeffa Chimoto -'' Ine Si wa sataniki'' kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi Billionare

Описание к видео Skeffa Chimoto -'' Ine Si wa sataniki'' kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi Billionare

Kupatula kuyimba, Skeffa amapangano ma business. Iyeyu ali ndi MAGalimoto ambiri omwe amanyamula katundu . Mu kanthawi kena, anayamba kutchuka ndi mbiri yosakhala bwino yoti iyeyu ndi mmodzi wa anthu a Satanic ndziko lino.

kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi mponda matiki
from sellingTsotsi Hat to a multi-millionaire
the story of skeffa chimoto

Комментарии

Информация по комментариям в разработке