Mudziko Muno Mulibe Chitetezo Phalombe Big Boy

Описание к видео Mudziko Muno Mulibe Chitetezo Phalombe Big Boy

On Nyasa VoiceBox, Phalombe Big Boy asserts that Malawi is not secure. He made this statement after a soldier was allegedly attacked by thieves within the boundaries of Cobbe Barracks in Zomba.


Pa Nyasa VoiceBox, Phalombe Big Boy wanenetsa kuti dziko la Malawi silili bwino. Iye wanena izi msilikali wina yemwe ati anamenyedwa ndi mbava m’malire a Cobbe Barracks ku Zomba.

#malawi

Комментарии

Информация по комментариям в разработке